12 Kenako Yehova anauza Satana kuti: “Chabwino, chilichonse chimene ali nacho chili mʼmanja mwako. Koma dzanja lako lisakhudze munthuyo.” Zitatero Satana anachoka pamaso pa Yehova.+
9 Zimenezi zikusonyeza kuti Yehova* amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasunga kuti adzawawononge pa tsiku lopereka chiweruzo,+