Aroma 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiponso amati: “Tamandani Yehova,* inu mitundu yonse ya anthu ndipo anthu onse amutamande.”+