Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Mphamvu ndi nyonga zanga ndi Ya,* chifukwa wandipulumutsa.+

      Ameneyu ndi Mulungu wanga ndipo ndidzamʼtamanda.+ Ndi Mulungu wa bambo anga,+ ndipo ndidzamulemekeza.+

  • Salimo 18:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+

      Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,

      Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+

  • Yesaya 12:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Taonani! Mulungu ndi chipulumutso changa.+

      Ndidzamukhulupirira ndipo sindidzaopa chilichonse,+

      Chifukwa Ya,* Yehova, ndi mphamvu zanga komanso nyonga zanga,

      Ndipo iye wakhala chipulumutso changa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena