1 Samueli 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova adzawononga onse olimbana naye,*+Akadzawakwiyira, kumwamba kudzagunda mabingu.+ Yehova adzaweruza dziko lonse lapansi,+Iye adzapereka mphamvu kwa mfumu yake,+Ndipo adzakweza nyanga* ya wodzozedwa wake.”+ 1 Samueli 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamene Samueli ankapereka nsembe yopsereza, Afilisiti anali akuyandikira kuti amenyane ndi Isiraeli. Zitatero, Yehova anachititsa mabingu amphamvu kwambiri+ pa tsiku limenelo kuti asokoneze+ Afilisiti. Choncho Afilisitiwo anagonjetsedwa ndi Aisiraeli.+
10 Yehova adzawononga onse olimbana naye,*+Akadzawakwiyira, kumwamba kudzagunda mabingu.+ Yehova adzaweruza dziko lonse lapansi,+Iye adzapereka mphamvu kwa mfumu yake,+Ndipo adzakweza nyanga* ya wodzozedwa wake.”+
10 Pamene Samueli ankapereka nsembe yopsereza, Afilisiti anali akuyandikira kuti amenyane ndi Isiraeli. Zitatero, Yehova anachititsa mabingu amphamvu kwambiri+ pa tsiku limenelo kuti asokoneze+ Afilisiti. Choncho Afilisitiwo anagonjetsedwa ndi Aisiraeli.+