Salimo 119:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndimasangalala ndi zikumbutso zanu,+Kuposa mmene ndimasangalalira ndi zinthu zina zonse zamtengo wapatali.+ Salimo 119:168 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 168 Ndimasunga malamulo anu ndi zikumbutso zanu,Chifukwa inu mukudziwa zinthu zonse zimene ndimachita.+
14 Ndimasangalala ndi zikumbutso zanu,+Kuposa mmene ndimasangalalira ndi zinthu zina zonse zamtengo wapatali.+
168 Ndimasunga malamulo anu ndi zikumbutso zanu,Chifukwa inu mukudziwa zinthu zonse zimene ndimachita.+