Salimo 86:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndilangizeni inu Yehova, za njira yanu.+ Kuti ndiyende mʼchoonadi chanu.+ Ndithandizeni kuti ndiziopa dzina lanu ndi mtima wonse.*+
11 Ndilangizeni inu Yehova, za njira yanu.+ Kuti ndiyende mʼchoonadi chanu.+ Ndithandizeni kuti ndiziopa dzina lanu ndi mtima wonse.*+