Salimo 141:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musalole kuti mtima wanga uzikonda chinthu chilichonse choipa,+Komanso kuti ndizichita zinthu zoipa limodzi ndi anthu oipa.Sindikufuna kudya chakudya chawo chapamwamba. Miyambo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zinthu zabodza komanso mawu onama muziike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma. Mungondipatsa chakudya chokwanira,+
4 Musalole kuti mtima wanga uzikonda chinthu chilichonse choipa,+Komanso kuti ndizichita zinthu zoipa limodzi ndi anthu oipa.Sindikufuna kudya chakudya chawo chapamwamba.
8 Zinthu zabodza komanso mawu onama muziike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma. Mungondipatsa chakudya chokwanira,+