Salimo 118:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nditavutika ndinaitana Ya.*Ya anandiyankha nʼkundipititsa pamalo otetezeka.*+