Yobu 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sindinasiye kutsatira malamulo otuluka pakamwa pake. Ndasunga mosamala mawu ake+ kuposa zimene amafuna kuti ndichite.* Salimo 119:174 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 174 Ndikulakalaka chipulumutso chanu, inu Yehova,Ndipo ndimakonda kwambiri chilamulo chanu.+ Aroma 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumtima mwanga ndimasangalala kwambiri ndi malamulo a Mulungu,+
12 Sindinasiye kutsatira malamulo otuluka pakamwa pake. Ndasunga mosamala mawu ake+ kuposa zimene amafuna kuti ndichite.*