Salimo 119:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ngakhale pamene akalonga asonkhana pamodzi nʼkumakambirana zoti andiukire,Ine mtumiki wanu ndimaganizira mozama* malangizo anu. Salimo 119:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Zili bwino kuti ndakumana ndi mavuto,+Kuti ndiphunzire malamulo anu.
23 Ngakhale pamene akalonga asonkhana pamodzi nʼkumakambirana zoti andiukire,Ine mtumiki wanu ndimaganizira mozama* malangizo anu.