Salimo 119:158 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 158 Ndimanyansidwa ndi anthu ochita zinthu mwachinyengo,Chifukwa sasunga mawu anu.+ Salimo 139:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu,+Ndipo ndimanyansidwa ndi anthu amene amakupandukirani.+ Miyambo 28:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu amene asiya chilamulo amatamanda munthu woipa,Koma amene amasunga chilamulo amakwiyira anthu amene asiya chilamulowo.+
21 Inu Yehova, pajatu ine ndimadana ndi anthu amene amadana nanu,+Ndipo ndimanyansidwa ndi anthu amene amakupandukirani.+
4 Anthu amene asiya chilamulo amatamanda munthu woipa,Koma amene amasunga chilamulo amakwiyira anthu amene asiya chilamulowo.+