Salimo 86:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Yehova ndinu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+Mumasonyeza chikondi chokhulupirika chochuluka kwa onse amene amaitana inu.+ Maliko 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yesu anamuyankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+
5 Inu Yehova ndinu wabwino+ ndipo ndinu wokonzeka kukhululuka.+Mumasonyeza chikondi chokhulupirika chochuluka kwa onse amene amaitana inu.+
18 Yesu anamuyankha kuti: “Nʼchifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino? Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+