Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimasangalala* kuchita zimene mumafuna, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+ Aroma 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mumtima mwanga ndimasangalala kwambiri ndi malamulo a Mulungu,+
8 Ndimasangalala* kuchita zimene mumafuna, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+