1 Mbiri 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso mphamvu zotsogolera Aisiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+ Yobu 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mzimu umene uli mwa anthu,Mpweya wa Wamphamvuyonse, ndi umene umawathandiza kuti azimvetsa zinthu.+
12 Yehova akupatse nzeru ndi kuzindikira.+ Akupatsenso mphamvu zotsogolera Aisiraeli, kuti usunge chilamulo cha Yehova Mulungu wako.+
8 Koma mzimu umene uli mwa anthu,Mpweya wa Wamphamvuyonse, ndi umene umawathandiza kuti azimvetsa zinthu.+