Salimo 119:147 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 147 Ndadzuka mʼbandakucha kuti ndipemphe thandizo kwa inu,+Chifukwa mawu anu ndi chiyembekezo changa.*
147 Ndadzuka mʼbandakucha kuti ndipemphe thandizo kwa inu,+Chifukwa mawu anu ndi chiyembekezo changa.*