Salimo 119:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zikanakhala bwino ndikanakhala wolimba*+Kuti nditsatire malangizo anu. 6 Zikanatero sindikanachita manyazi,+Pa nthawi imene ndikuganizira malamulo anu onse. 1 Yohane 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Tsopano inu ana anga okondedwa, khalanibe ogwirizana naye kuti akadzaonekera, tidzakhale ndi ufulu wa kulankhula.+ Komanso kuti tisadzachoke pamaso pake mwamanyazi pa nthawi ya kukhalapo* kwake.
5 Zikanakhala bwino ndikanakhala wolimba*+Kuti nditsatire malangizo anu. 6 Zikanatero sindikanachita manyazi,+Pa nthawi imene ndikuganizira malamulo anu onse.
28 Tsopano inu ana anga okondedwa, khalanibe ogwirizana naye kuti akadzaonekera, tidzakhale ndi ufulu wa kulankhula.+ Komanso kuti tisadzachoke pamaso pake mwamanyazi pa nthawi ya kukhalapo* kwake.