Salimo 119:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Zingwe za oipa zandikulunga,Koma ine sindinaiwale chilamulo chanu.+ Salimo 119:176 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 176 Ndasochera ngati nkhosa yotayika.+ Ndifunefuneni ine mtumiki wanu,Chifukwa sindinaiwale malamulo anu.+
176 Ndasochera ngati nkhosa yotayika.+ Ndifunefuneni ine mtumiki wanu,Chifukwa sindinaiwale malamulo anu.+