Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Nyamukani mutakwiya, inu Yehova.

      Imirirani ndi kukhaulitsa adani anga amene andikwiyira.+

      Dzukani nʼkundithandiza, ndipo mulamule kuti chilungamo chichitike.+

  • Chivumbulutso 6:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Atamatula chidindo cha 5, ndinaona pansi pa guwa lansembe+ pali miyoyo*+ ya anthu amene anaphedwa chifukwa cha mawu a Mulungu ndiponso chifukwa cha ntchito yochitira umboni.+ 10 Iwo anafuula ndi mawu okweza akuti: “Mudzalekerera mpaka liti, inu Ambuye Wamkulu Koposa, Mulungu woyera ndi woona,+ osaweruza ndi kubwezera okhala padziko lapansi chifukwa cha magazi athu?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena