Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+ Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Miyambo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chifukwa Yehova ndi amene amapereka nzeru.+Kudziwa zinthu komanso kuzindikira zimatuluka mʼkamwa mwake. Miyambo 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Munthu wanzeru mumtima mwake amamvera malangizo,*+Koma wolankhula mopusa adzapeza mavuto.+
7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+ Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
6 Chifukwa Yehova ndi amene amapereka nzeru.+Kudziwa zinthu komanso kuzindikira zimatuluka mʼkamwa mwake.