46 Ndiyeno patatha masiku atatu, anamupeza ali mʼkachisi, atakhala pakati pa aphunzitsi ndipo ankawamvetsera nʼkumawafunsa mafunso. 47 Koma onse amene ankamumvetsera anadabwa kwambiri ndi mayankho ake komanso poona kuti anali womvetsa zinthu kwambiri.+