Salimo 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzakhalabe wosalakwa pamaso pake,+Ndipo ndidzayesetsa kupewa cholakwa.+ Salimo 119:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Ndaganizira mozama za njira zanga,Kuti mapazi anga ndiwabwezere ku zikumbutso zanu.+