Salimo 97:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+ Salimo 101:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Sindidzayangʼana chinthu chilichonse choipa.* Ndimadana ndi zochita za anthu amene asiya kuchita zinthu zabwino.+Sindidzalola kuti zochita zawozo zindikhudze. Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+ Miyambo 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wolungama amadana ndi mabodza,+Koma zochita za munthu woipa zimabweretsa manyazi ndi kunyozeka. Aroma 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chikondi chanu chisakhale chachiphamaso.+ Muzinyansidwa ndi zoipa+ nʼkumayesetsa kuchita zabwino.
10 Inu amene mumakonda Yehova, muzidana ndi zoipa.+ Iye amateteza moyo wa anthu ake okhulupirika.+Amawapulumutsa mʼmanja mwa* oipa.+
3 Sindidzayangʼana chinthu chilichonse choipa.* Ndimadana ndi zochita za anthu amene asiya kuchita zinthu zabwino.+Sindidzalola kuti zochita zawozo zindikhudze.
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso mawu achinyengo.+