Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 50:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Amene akundiyamikira kuti ikhale nsembe imene akupereka kwa ine akundilemekeza.+

      Ndipo munthu amene akupitiriza kuchita zabwino,

      Ndidzamuonetsa chipulumutso changa.”+

  • Hoseya 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Bwererani kwa Yehova ndi mawu amenewa.

      Uzani Mulungu kuti, ‘Tikhululukireni zolakwa zathu.+ Landirani zinthu zathu zabwino,

      Ndipo tidzakutamandani ndi pakamwa pathu+ ngati mmene tingaperekere nsembe kwa inu ana a ngʼombe amphongo.

  • Aheberi 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu kudzera mwa Yesu.+ Kuchita zimenezi kuli ngati nsembe imene tikupereka kwa Mulungu ndipo timagwiritsa ntchito milomo yathu+ polengeza dzina lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena