Deuteronomo 33:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+ Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+ Yesaya 48:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova, Wokuwombolani, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu,Amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,*+Amene ndimakutsogolerani mʼnjira imene mukuyenera kuyenda.+
10 Amenewa azilangiza Yakobo pa zigamulo zanu+Ndi Isiraeli mʼChilamulo chanu.+ Azipereka nsembe zofukiza kuti zikhale kafungo kosangalatsa kwa inu,*+Ndi nsembe yathunthu paguwa lanu lansembe.+
17 Yehova, Wokuwombolani, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Ine Yehova ndine Mulungu wanu,Amene ndimakuphunzitsani kuti zinthu zikuyendereni bwino,*+Amene ndimakutsogolerani mʼnjira imene mukuyenera kuyenda.+