Salimo 40:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimasangalala* kuchita zimene mumafuna, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+ Salimo 119:97 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 97 Ndimakonda kwambiri chilamulo chanu!+ Ndimaganizira mozama* chilamulocho tsiku lonse.+
8 Ndimasangalala* kuchita zimene mumafuna, inu Mulungu wanga,+Ndipo chilamulo chanu chili mumtima mwanga.+