Salimo 119:81 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 81 Ine ndikulakalaka chipulumutso chanu,+Chifukwa mawu anu ndi chiyembekezo changa.*