Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+ Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Miyambo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Miyambi ya Solomo+ mwana wa Davide,+ mfumu ya Isiraeli:+ Miyambo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yothandiza munthu wosadziwa zinthu kuti akhale wozindikira.+Yothandiza wachinyamata kuti akhale wodziwa zinthu komanso kuti aziganiza bwino.+ 2 Timoteyo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera+ amene angakupatse nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke chifukwa chokhulupirira Khristu Yesu.+
7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+ Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
4 Yothandiza munthu wosadziwa zinthu kuti akhale wozindikira.+Yothandiza wachinyamata kuti akhale wodziwa zinthu komanso kuti aziganiza bwino.+
15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera+ amene angakupatse nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke chifukwa chokhulupirira Khristu Yesu.+