Aheberi 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa Mulungu si wosalungama kuti angaiwale ntchito yanu ndiponso chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ potumikira oyera ndipo mukupitiriza kuwatumikira.
10 Chifukwa Mulungu si wosalungama kuti angaiwale ntchito yanu ndiponso chikondi chimene munachisonyeza pa dzina lake,+ potumikira oyera ndipo mukupitiriza kuwatumikira.