Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Yehova anauza munthu uja kuti: “Uyendeyende mumzinda wonse wa Yerusalemu ndipo ulembe chizindikiro pazipumi za anthu amene akuusa moyo komanso kubuula+ chifukwa cha zonyansa zonse zimene zikuchitika mumzindawu.”+

  • 2 Petulo 2:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma anapulumutsa Loti yemwe anali munthu wolungama.+ Loti ankavutika kwambiri mumtima chifukwa cha khalidwe lopanda manyazi* limene anthu ophwanya malamulo ankachita. 8 (Munthu wolungamayu ankavutika mumtima tsiku ndi tsiku chifukwa cha zimene ankaona ndiponso kumva pamene ankakhala pakati pa anthu oipa. Iye ankavutika mumtima chifukwa cha zochita zawo zosamvera malamulo.)

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena