2 Mafumu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anamuuza kuti: “Tiye tipitire limodzi ukaone kuti sindilekerera zoti anthu azipikisana* ndi Yehova.”+ Choncho Yehonadabu anapita limodzi ndi anthuwo mʼgaleta lankhondo la Yehu. Salimo 69:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kudzipereka kwanga panyumba yanu kuli ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga,+Ndipo chipongwe cha anthu amene amakunyozani chandigwera.+ Yohane 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena kuti: “Kudzipereka kwanga panyumba yanu kudzakhala ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga.”+
16 Kenako anamuuza kuti: “Tiye tipitire limodzi ukaone kuti sindilekerera zoti anthu azipikisana* ndi Yehova.”+ Choncho Yehonadabu anapita limodzi ndi anthuwo mʼgaleta lankhondo la Yehu.
9 Kudzipereka kwanga panyumba yanu kuli ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga,+Ndipo chipongwe cha anthu amene amakunyozani chandigwera.+
17 Ophunzira ake anakumbukira zimene Malemba amanena kuti: “Kudzipereka kwanga panyumba yanu kudzakhala ngati moto umene ukuyaka mumtima mwanga.”+