Salimo 22:6, 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ine ndine nyongolotsi osati munthu,Anthu amandinyogodola* komanso kundinyoza.+ 7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+
6 Koma ine ndine nyongolotsi osati munthu,Anthu amandinyogodola* komanso kundinyoza.+ 7 Anthu onse amene amandiona amandiseka.+Iwo amandinyogodola nʼkumapukusa mitu yawo mondinyoza nʼkumati:+