-
Salimo 119:40Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
40 Taonani mmene ndikulakalakira malamulo anu.
Ndithandizeni kukhalabe ndi moyo mogwirizana ndi chilungamo chanu.
-
-
Salimo 119:88Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
88 Ndithandizeni kuti ndikhalebe ndi moyo chifukwa cha chikondi chanu chokhulupirika,
Kuti ndisunge zikumbutso zimene mwatipatsa.
-