2 Samueli 7:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, ndinu Mulungu woona ndipo mawu anu ndi oona,+ komanso mwandilonjeza ine mtumiki wanu zinthu zabwinozi. Salimo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mawu a Yehova ndi oyera.+Ali ngati siliva woyengedwa mungʼanjo yadothi nthawi zokwanira 7. Yohane 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ayeretseni* pogwiritsa ntchito choonadi.+ Mawu anu ndi choonadi.+
28 Inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, ndinu Mulungu woona ndipo mawu anu ndi oona,+ komanso mwandilonjeza ine mtumiki wanu zinthu zabwinozi.