-
Salimo 27:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Tsopano ndapambana pamaso pa adani anga onse amene andizungulira.
Ndidzapereka nsembe patenti yake ndikufuula mosangalala.
Ndidzaimba nyimbo zotamanda Yehova.
-