Yesaya 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo sadzakhala ndi njala ndipo sadzamva ludzu,+Komanso sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Chifukwa amene amawachitira chifundo adzawatsogolera+Ndipo adzapita nawo kumene kuli akasupe amadzi.+ Chivumbulutso 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo sadzamvanso njala kapena ludzu. Dzuwa kapena kutentha kulikonse sikudzawawotcha,+
10 Iwo sadzakhala ndi njala ndipo sadzamva ludzu,+Komanso sadzamva kutentha kapena kupsa ndi dzuwa.+ Chifukwa amene amawachitira chifundo adzawatsogolera+Ndipo adzapita nawo kumene kuli akasupe amadzi.+