1 Mafumu 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawiyi mʼpamene Solomo anamangira Kemosi malo okwezeka.+ Kemosi anali mulungu wonyansa wa Amowabu ndipo anamʼmangira malowo paphiri lomwe linali pafupi ndi Yerusalemu. Anamangiranso Moleki,+ mulungu wonyansa wa Aamoni,+ malo okwezeka. Machitidwe 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anabwerera ku Yerusalemu,+ kuchokera kuphiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*
7 Pa nthawiyi mʼpamene Solomo anamangira Kemosi malo okwezeka.+ Kemosi anali mulungu wonyansa wa Amowabu ndipo anamʼmangira malowo paphiri lomwe linali pafupi ndi Yerusalemu. Anamangiranso Moleki,+ mulungu wonyansa wa Aamoni,+ malo okwezeka.
12 Kenako anabwerera ku Yerusalemu,+ kuchokera kuphiri la Maolivi. Phiri limeneli lili pafupi ndi Yerusalemu, pa mtunda wa ulendo wa tsiku la sabata.*