Salimo 130:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Isiraeli apitirize kuyembekezera Yehova,Chifukwa Yehova amasonyeza chikondi chokhulupirika,+Ndipo ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu. Mika 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzayembekezera Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+
7 Isiraeli apitirize kuyembekezera Yehova,Chifukwa Yehova amasonyeza chikondi chokhulupirika,+Ndipo ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu.
7 Koma ine ndidzayembekezera Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+