1 Mafumu 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komabe, chifukwa cha kukhulupirika kwa Davide,+ Yehova Mulungu wake anamʼpatsa nyale mu Yerusalemu+ pokweza mwana wake pambuyo pake ndiponso pochititsa kuti Yerusalemu akhalepobe. 2 Mafumu 19:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “Ndidzateteza mzindawu+ ndipo ndidzaupulumutsa chifukwa cha ineyo+Ndiponso chifukwa cha mtumiki wanga Davide.”’”+
4 Komabe, chifukwa cha kukhulupirika kwa Davide,+ Yehova Mulungu wake anamʼpatsa nyale mu Yerusalemu+ pokweza mwana wake pambuyo pake ndiponso pochititsa kuti Yerusalemu akhalepobe.
34 “Ndidzateteza mzindawu+ ndipo ndidzaupulumutsa chifukwa cha ineyo+Ndiponso chifukwa cha mtumiki wanga Davide.”’”+