-
1 Mbiri 9:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Amenewa anali oimba, atsogoleri a nyumba za makolo a Alevi mʼzipinda zodyera. Iwo sankapatsidwa ntchito zina chifukwa ankagwira ntchito yawo masana komanso usiku.
-
-
1 Mbiri 23:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Chifukwa mogwirizana ndi malangizo omaliza a Davide, Alevi oyambira zaka 20 kupita mʼtsogolo, anawerengedwa.
-
-
Luka 2:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Tsopano anali mkazi wamasiye ndipo anali ndi zaka 84 koma sankasowa pakachisi. Ankachita utumiki wopatulika masana ndi usiku ndipo ankasala kudya komanso kupemphera mopembedzera.
-