Genesis 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho Mulungu anapanga zounikira ziwiri. Chounikira chowala kwambiri anachipanga kuti chiziwala* masana,+ ndipo chowala pangʼono kuti chiziwala* usiku, komanso anapanga nyenyezi.+ Yeremiya 31:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yehova amene amapereka dzuwa kuti liziwala masana,Amene amaika malamulo oti mwezi ndi nyenyezi ziziwala usiku,Amene amavundula nyanjaKuti mafunde ake achite phokoso,Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti:+
16 Choncho Mulungu anapanga zounikira ziwiri. Chounikira chowala kwambiri anachipanga kuti chiziwala* masana,+ ndipo chowala pangʼono kuti chiziwala* usiku, komanso anapanga nyenyezi.+
35 Yehova amene amapereka dzuwa kuti liziwala masana,Amene amaika malamulo oti mwezi ndi nyenyezi ziziwala usiku,Amene amavundula nyanjaKuti mafunde ake achite phokoso,Amene dzina lake ndi Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, wanena kuti:+