Yesaya 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka.Phokoso la anthu amene akusangalala latha.Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze sizikumvekanso.+
8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka.Phokoso la anthu amene akusangalala latha.Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze sizikumvekanso.+