Salimo 123:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu odzikuza atinyoza kwambiri*Ndipo anthu onyada atichitira zachipongwe.