Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 47:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Tsika ukhale pafumbi

      Iwe namwali, mwana wamkazi wa Babulo.*+

      Ukhale padothi pomwe palibe mpando wachifumu,+

      Iwe mwana wamkazi wa Akasidi,

      Chifukwa anthu sadzakutchulanso kuti ndiwe wolekereredwa ndiponso wosasatitsidwa.

  • Yeremiya 25:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 ‘Ndiyeno zaka 70 zimenezo zikadzakwana,+ ndidzalanga mfumu ya Babulo ndi mtundu umenewo chifukwa cha zolakwa zawo.+ Ndipo dziko la Akasidi ndidzalisandutsa bwinja mpaka kalekale,’ akutero Yehova.+

  • Yeremiya 50:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 “Nenani ndi kulengeza zimene zachitika kwa anthu a mitundu ina.

      Imikani mtengo wachizindikiro ndipo lengezani zimenezi.

      Musabise chilichonse.

      Nenani kuti, ‘Babulo walandidwa.+

      Beli wachititsidwa manyazi.+

      Merodaki wachita mantha.

      Mafano a Babulo achititsidwa manyazi.

      Mafano ake onyansawo* achita mantha.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena