1 Samueli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyale ya Mulungu+ inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona mʼkachisi*+ wa Yehova mmene munali Likasa la Mulungu. 1 Mbiri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anabweretsa Likasa la Mulungu woona pamalo amene Davide anakonza nʼkuliika mutenti imene iye anamanga kuti lizikhalamo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano kwa Mulungu woona.+ Salimo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+
3 Nyale ya Mulungu+ inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona mʼkachisi*+ wa Yehova mmene munali Likasa la Mulungu.
16 Choncho anabweretsa Likasa la Mulungu woona pamalo amene Davide anakonza nʼkuliika mutenti imene iye anamanga kuti lizikhalamo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano kwa Mulungu woona.+
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+