Salimo 18:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Iye amandipulumutsa kwa adani anga olusa.Mumandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mumandipulumutsa kwa munthu wachiwawa. Salimo 59:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Inu Mulungu wanga, ndipulumutseni kwa adani anga.+Nditetezeni kwa anthu amene akundiukira.+
48 Iye amandipulumutsa kwa adani anga olusa.Mumandikweza pamwamba pa anthu amene amandiukira.+Mumandipulumutsa kwa munthu wachiwawa.