Salimo 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amadikirira anthu pamalo amene iye amabisala ngati mkango umene uli pamalo ake amene umabisala.*+ Amadikirira kuti agwire munthu wovutika. Amagwira munthu wovutikayo pomukulunga ndi ukonde wake.+
9 Amadikirira anthu pamalo amene iye amabisala ngati mkango umene uli pamalo ake amene umabisala.*+ Amadikirira kuti agwire munthu wovutika. Amagwira munthu wovutikayo pomukulunga ndi ukonde wake.+