Yeremiya 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mʼnyumba zawo mumveke kuliraMukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi. Chifukwa akumba dzenje kuti andigwireNdipo atchera misampha kuti akole mapazi anga.+
22 Mʼnyumba zawo mumveke kuliraMukawabweretsera magulu achifwamba mwadzidzidzi. Chifukwa akumba dzenje kuti andigwireNdipo atchera misampha kuti akole mapazi anga.+