Salimo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+ Salimo 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu Mulungu, mvetserani pemphero langa,+Ndipo musanyalanyaze pempho langa lakuti mundichitire chifundo.*+
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+
55 Inu Mulungu, mvetserani pemphero langa,+Ndipo musanyalanyaze pempho langa lakuti mundichitire chifundo.*+