Salimo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mavuto amene akuwayambitsawo adzabwerera pamutu pake,+Zinthu zachiwawa zimene akuchita zidzagwera paliwombo pake. Miyambo 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu woipa amakodwa ndi zolankhula zake zochimwa,+Koma wolungama amapulumuka pamavuto.
16 Mavuto amene akuwayambitsawo adzabwerera pamutu pake,+Zinthu zachiwawa zimene akuchita zidzagwera paliwombo pake.