Salimo 11:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amayangʼanitsitsa munthu wolungama komanso munthu woipa.+Mulungu amadana ndi aliyense amene amakonda chiwawa.+ 6 Oipa, iye adzawagwetsera misampha* ngati mvula.Moto ndi sulufule+ komanso mphepo yotentha zidzakhala chakumwa chawo.
5 Yehova amayangʼanitsitsa munthu wolungama komanso munthu woipa.+Mulungu amadana ndi aliyense amene amakonda chiwawa.+ 6 Oipa, iye adzawagwetsera misampha* ngati mvula.Moto ndi sulufule+ komanso mphepo yotentha zidzakhala chakumwa chawo.